Qur'an ya Chichewa offline ikupezeka tsopano pa internet.
Ili ndi ndemanga pansi apo ndi apo.
Ndipo theka la Qur'an imeneyi lili mu Chichewa chokhachokha, pomwe theka linali lili ndi Arabic pansi pa Chichewa.
Izi zachitika Pofuna kuthandiza ma Daiy omwe akupanga Da'wah mma social media komanso awo omwe sabva Arabic.
Ndipo kwa ma Daiy yafewetsedwa motere:
Ndiyotheka kuipanga copy and paste kuti pasakhale kulemba chimodzichimodzi. (Just long click to copy and paste)
Komanso mutha kumutumizira munthu wina app imeneyi kudzera mkati mwa App yomweyi.